I've been low nthawi yaitali
Mene ndinkavutika kunalibeko
I've been down nthawi yaitali
Mene ndinkazuzika kunalibeko iwe
Uwauze
Choka ungandibele shine
Ungandibele shine
Ndamuuza
(Choka ungandibele shine, Ungandibele shine)
Ungandibele shine
(Ungandibele shine)
Shine
(Ungandibele shine)
Ungandibele shine
(Ungandibele shine)
Shine
(Ungandibele shine)
Amakukonda akakhala mavuto
Zawo zikamayenda amakuika pambali
Amakukonda pamaso
Kumbali akuku konzela maupo
Nde munthu nde munthuyo
Sungamvetsetse
Anzawo akuphusha
Ali busy ku hater
Pano zawo zikuyenda
Iwo alibe chochitabe
Ali busy magulu magulu kunyoza anzawo
Musawatengele iwe sumadya kwawo
I've been low nthawi yaitali
Mene ndinkavutika kunalibeko
(Kunalibeko)
I've been down nthawi yaitali
Mene ndinkazuzika kunalibeko iwe
Uwauze
Choka ungandibele shine
Ungandibele shine
Ndamuuza
(Choka ungandibele shine, Ungandibele shine)
Ungandibele shine
(Ungandibele shine)
Shine
(Ungandibele shine)
Ungandibele shine
(Ungandibele shine)
Shine
(Ungandibele shine)
Amafuna ukhale pa low
Iwo ziziwayendelabe
Samafuna uzioneka bho
They always pray for your downfall
Iwo samakufunila zabwino
Angofuna ufe
Angofuna ugwe
Uvutike
Koma, anzawo akuphusha
Ali busy ku hater
Pano zawo zikuyenda
Iwo alibe chochitabe
Ali busy magulu magulu kunyoza anzawo
Usawatengele iwe sumadya kwawo
I've been low nthawi yaitali
(Nthawi yaitali
Mene ndinkavutika knalibeko
(Kunalibeko)
I've been down nthawi yaitali
(Nthawi yaitali)
Mene ndinkazuzika kunalibeko iwe
Uwauze
Choka ungandibele shine
Ungandibele shine
Ndamuuza
(Choka ungandibele shine Ungandibele shine)
Ungandibele shine
(Ungandibele shine)
Shine
(Ungandibele shine)
Ungandibele shine
(Ungandibele shine)
Shine
(Ungandibele shine)