Eeeeh, uledzeli, chokumwa
Mwana olowelela lero yard sakuvaya
G sakugwilika ine ndi live wire
Got a drunken master, dolo vibe on fire
Mwene phere, mbiyang'ambi, wakunimanya muchikaya
Kuli wankhuni ndikumene timatchila
Ngati dzana masana, dzulo madzulo
Lero lino komanso mawa mammawa
Wanna chill with the Don, you'll know were the boy be
Mphala yanga sungailowe chamutu
Ndimavunga ma puch, kenako mateche
Deep love for the booz ngati nyanja yaku Chintheche
Ndikamamwa ndekha venta imakhala mphechepeche
Wankhuni tikuyaka uleke utsi ufuke
Nkazi oyaluka ileke skirt ivuke
Ugudumuke, usupuke mpakaka bawa isungunuke
We go do it again mawa, ndizomwe timakonda
Ndikayaka ndimafila
Zodabadika, kudya staga nkamabang'a zimandiwaza
Ndikayaka ndimafila aise
Ndikayaka ndimafila, ndimafila, ndimaupeza
Ngati dzulo inalakwa lero nde ikhala worse
Kustager two steps ndikudzadya ka revers
Dzulo n'nachoka chozemba lero ndichita kukwawa
Uledzeli dongosolo is every day all day
I some times think bawa inandidyetsa konda ine
Kuchita kulimbikila ngati ndifuna ndiwine
Kuyaka, kublanda, kublaka ndikati ndithime
All over the place nkati ndiime ndivine
Ine nkhani yachokumwa ndi madala
Big league, ya'll know am a baller
Kupanda kutenga masipi ndimadwala
Take it katatu patsiku ngati dose yamankhwala
Kundikhola kopanda bawa sindifika ngati mawa
Ine sober kuledzela kwawina nditha kukawa
Best friend wanga mowa, girlfriend mowa
M'bale okonda m'mavuto pantendere, mowa
Ndikayaka ndimafila
Zodabadika, kudya staga nkamabang'a zimandiwaza
Ndikayaka ndimafila aise
Ndikayaka ndimafila, ndimafila, ndimaupeza
Ndikayaka ndimafila
Zodabadika, kudya staga nkamabang'a zimandiwaza
Ndikayaka ndimafila aise
Ndikayaka ndimafila, ndimafila, ndimaupeza