Ineyo
Ineyo
Iweyo
Ifeyo
Ineyo
Iweyoo
Iweyo
Ndatopa ndikulila ine
Ndikufuna nditamanyadila ine
Ine makufila umaziwa iwe
Koma sumafuna kundiika mu game
Ukafuna chats timatchillla ife
Ukafuna nthawi makupasa ine
Zingavute bwanji umafila iwe
Koma umasintha iwe
Umatripper iwe
Bwanji umatripper iwe
Kodi nanga bwanji umatripper iwe
Umatripper iwe
Ukutripper iwe
Kodi nanga bwanji ukutripper iwe
Tandiuze bwanji ukutripper iwe
Ukutripper iwe
Ey
Ukutripper iwe
Kukhala ndi anzako kumasimbwa iwe
Kufuna kukuhala kumazemba iwe
Kukumana ku stunners kundiskipper ine
You gave me one call and now im standing right here
Im prolly in love that's how i'm feeling right here
Lemme take off all your clothes and lets just do it right here
We aint even a thing but all we do is fight here
And i'm prolly in a bottle cause i dont get it
Just tell me right now yeah i'm done waiting
I know you got a broken heart let me mend it
I know you a problem but you need saving
Now i drown in a bottle cause this shit draining
I just pour up cause its been raining
Took a shot straight to my heart you got aiming
I know im not perfect but I dont deserve this Nah
Ndatopa ndikulila ine
Ndikufuna nditamanyadila ine
Ine makufila umaziwa iwe
Koma sumafuna kundiika mu game
Ukafuna chats timatchillla ife
Ukafuna nthawi makupasa ine
Zingavute bwanji umafila iwe
Koma umasintha iwe
Umatripper iwe
Bwanji umatripper iwe
Kodi nanga bwanji umatripper iwe
Umatripper iwe
Ukutripper iwe
Kodi nanga bwanji ukutripper iwe
Tandiuze bwanji ukutripper iwe
Ukutripper iwe