How do you deal with stress and sadness in your life
Mtima ukuwawa, mafuso sakukata
Life seems to be a mystery to solve
Anthu akuvaya uko kunsabwera
Kuyanga'ana mtendere, the world cannot give
Kodi ndichisankho? Kapena kusweka kwa muntima
Ichi ndichilaso, ndigwira mtengo wanji
Notes sanasiye, wasiya umasiye
Ndipanga nawo chani makanda sanakule
Anthu akuzipha Ine sinkuvetsa
Ana ang'ono, akulu ndi agogo
Kodi ndiajaje kapena ndiamvetse
Mwina singavetse makutu ndiatseke
Nanga ndichiyani mavuto agwera tonse
Mwina pali pena pomwe singaziwe
Nkhani ikuvuta thandizeni ndziwe
Number one, worrying a lot all the time
Do you feel like you are in high alert all the time
Are you over worrying about things you can't control
If you are worrying and hurting more than usual, chances are
Your mental health is at risk
Worried that turns into become anxiety or may interfere with everyday life
When your mind is under siege with worry and fear
Mitima imasweka. Pena nkhawa imandipeza
Zoti akuzipha sinkhani yopeka chifukwa pena timaseka
Depression ilipo, aliyense ithakumutenga
Mfana mkulu, bambo mmayi msungwana anyamata
Aliyense afuna kuzikhweza
Mumtima akuti afuna akapulume
Mavuto achuluka afuna akapungule
Poti kwathu sipadziko. Nde mwina tingovomela
Poti afuna okha nde mwina tingololela
After all, ngini ikushupha
Prices are rising, ma BP ango shoota
Maybe it's justifiable
Who are we to judge? It's really undeniable
Poti sitidziwa kut zimakhala Bwanji
This can affect your personal relationships, life at work, and your motivation as well
Number two
Feeling guilty or worthless
You constantly think that you're a failure
Or think everything wrong that happens in your life is your fault
Feeling guilty and worthless are indicative of depression
You might have had very strict parents who had extremely high expectations
Or you might have been surrounded by a group of friends who constantly made you feel bad about yourself
Such interactions can heavily affect your mental health and self-esteem
Number three
Having difficulty readjusting to home or work life
Have you experienced a traumatic event and can't seem to readjust to your home or work life
Experiences such as the loss of a loved one or natural disasters
Can have an extremely negative impact on your psychological well-being