Back to Top

Don Intellect Shakur - Dziko (feat. Nefter) Lyrics



Don Intellect Shakur - Dziko (feat. Nefter) Lyrics
Official




Yeah yeaah
Ili ndi dziko
Dziko
Dziko
Oh my God Nefter
Kwacha
Dzulodzuloli m'nali bwana
Mponda makwacha
M'nali nawo abwezi, osayamba
Masana poyelayela
Bilimankhwe asintha mawanga
Lero m'kazi ndilibe wathawa
Poti ndalama ndilibe, andikawa
Akuseka ajawa
Ndinkati abale aja
Ondilimbikitsa ndajawa
Ndinkawanyoza aja
Abale anga
Ubale ndimpakampaka
Olo akudzale
Zinthu zimasintha abale
Pamsana panjovu paja umapatsika
Mame, umawasamba
Unkawathawa aja umawasaka
Sabale ako aja, umawafuna
Umkatafula, koma Osadziwa mawuwa
Dziko
Nlozongulira
Sintchito kuleza mtima
Sitchimo kupeza chuma
Koma mlomo sunga
Koma mlomo sunga
Mudzi ndi anthu
Umodzi mu anthu
Umamanga mudzi
Akulu adati
Akulu adati
Mutu umodzi suseza denga, mulipo angati
Mulipo angati
Okoma mawu ogonera, lero mwayamba ankatii
Ankati
Ankati
Osamaiwala zonse ndi nthawi
Ili ndi dziko
Dziko
Dziko
Chaona nzako chapita mawa pakhomo pako chidza
Mapazi siya pamene upaza sista
Chamawa sichidziwika
Mawa zinthu zitha kusintha
Mphawi lero
Mawa magalimoto uchita kusintha
Osapusitsika
Zamawa amadziwa ndi chauta
Kumbuka wakutsina khutu, ndi mnansi
Imva mawuwa
Dziko ndimambala osalidalira
Kumabwela dzuwa
Nthawi kukhala mabala
Momwe ulili kulira
Ukazemba, umakumana nchokwawa
Chagada mkuzima
Ngati pusi pothawa
Dziko mlozongulira
Moyo nkudengulira
Kupuma nkusamalitsa
Ndi njuga kupeza chuma
Nkukhuta kutaya nsima
Ndi phuma kunena nzako mphawi
Kukhwima mmutu ndi nzeru
Pachikondi chita machawi
Dziko mlozungulira
Osachita makani
Nkhani dekhani,, sinthani
Musanazikonde sinkhani sinkhani
Lemekeza chikondi osati udani
Osati udani
Mudzi ndi anthu
Umodzi mu anthu
Umamanga mudzi
Akulu adati
Akulu adati
Mutu umodzi suseza denga, mulipo angati
Mulipo angati
Okoma mawu ogonera, lero mwayamba ankati
Ankati
Ankati
Osamaiwala zonse ndi nthawi
Ili ndi dziko
Dziko
Dziko
Dziko
Ili ndi dziko
Dziko
Dziko
Dziko
[ Correct these Lyrics ]

[ Correct these Lyrics ]

We currently do not have these lyrics. If you would like to submit them, please use the form below.


We currently do not have these lyrics. If you would like to submit them, please use the form below.




Yeah yeaah
Ili ndi dziko
Dziko
Dziko
Oh my God Nefter
Kwacha
Dzulodzuloli m'nali bwana
Mponda makwacha
M'nali nawo abwezi, osayamba
Masana poyelayela
Bilimankhwe asintha mawanga
Lero m'kazi ndilibe wathawa
Poti ndalama ndilibe, andikawa
Akuseka ajawa
Ndinkati abale aja
Ondilimbikitsa ndajawa
Ndinkawanyoza aja
Abale anga
Ubale ndimpakampaka
Olo akudzale
Zinthu zimasintha abale
Pamsana panjovu paja umapatsika
Mame, umawasamba
Unkawathawa aja umawasaka
Sabale ako aja, umawafuna
Umkatafula, koma Osadziwa mawuwa
Dziko
Nlozongulira
Sintchito kuleza mtima
Sitchimo kupeza chuma
Koma mlomo sunga
Koma mlomo sunga
Mudzi ndi anthu
Umodzi mu anthu
Umamanga mudzi
Akulu adati
Akulu adati
Mutu umodzi suseza denga, mulipo angati
Mulipo angati
Okoma mawu ogonera, lero mwayamba ankatii
Ankati
Ankati
Osamaiwala zonse ndi nthawi
Ili ndi dziko
Dziko
Dziko
Chaona nzako chapita mawa pakhomo pako chidza
Mapazi siya pamene upaza sista
Chamawa sichidziwika
Mawa zinthu zitha kusintha
Mphawi lero
Mawa magalimoto uchita kusintha
Osapusitsika
Zamawa amadziwa ndi chauta
Kumbuka wakutsina khutu, ndi mnansi
Imva mawuwa
Dziko ndimambala osalidalira
Kumabwela dzuwa
Nthawi kukhala mabala
Momwe ulili kulira
Ukazemba, umakumana nchokwawa
Chagada mkuzima
Ngati pusi pothawa
Dziko mlozongulira
Moyo nkudengulira
Kupuma nkusamalitsa
Ndi njuga kupeza chuma
Nkukhuta kutaya nsima
Ndi phuma kunena nzako mphawi
Kukhwima mmutu ndi nzeru
Pachikondi chita machawi
Dziko mlozungulira
Osachita makani
Nkhani dekhani,, sinthani
Musanazikonde sinkhani sinkhani
Lemekeza chikondi osati udani
Osati udani
Mudzi ndi anthu
Umodzi mu anthu
Umamanga mudzi
Akulu adati
Akulu adati
Mutu umodzi suseza denga, mulipo angati
Mulipo angati
Okoma mawu ogonera, lero mwayamba ankati
Ankati
Ankati
Osamaiwala zonse ndi nthawi
Ili ndi dziko
Dziko
Dziko
Dziko
Ili ndi dziko
Dziko
Dziko
Dziko
[ Correct these Lyrics ]
Writer: Arnold Malata, Blessings Mtsiriza
Copyright: Lyrics © O/B/O DistroKid




Don Intellect Shakur - Dziko (feat. Nefter) Video
(Show video at the top of the page)

Tags:
No tags yet