Bag yanga ndimunthu, imakhuta mfwefwe
Gobo ndi ine sititchila, ndimateche
They say I spit shit, eya ndimaspita zikhawa
Me and Shakur tamva zoti, koza lero sikaza mawa
So it's Kay-Taii osamayesa ndikucheza
Nkakuikani mmadzi osamayesa mukugeza
Tinamva zoti tikamavutika mmaupeza
Chibwana eti mmadzi sitilemba timaweza
I don't speak to y'all, I speak to souls
Remenencing on how I made it with two balls
Empty with no nuts
Lost pounds put my trust in a wrong whore
Lost a lot more when my nigga was no more
Everything digital nkazi kugwirira MO
Pamutu wanzanu busy wamasuku mmemo
Tikadari ana tidakhwimira mavuto
Nde muzitiyankha tikabwera ndimafunso
I know you listening
Mfana ndimvetsetse
Mfana khala chete
Usakhalee ngat ntchentche
I know you listening
Mfana ndimvetsetse
Mfana khala chete
Usakhale ngat ntchentche
I heard you talking
Nigga you wanna know me
I heard you talking
Nigga you wanna know me
I know you listening
Mfana ndimvetsetse
Mfana khala chete
Usakhalee ngat ntchentche
I know you listening
Mfana ndimvetsetse
Mfana khala chete
Usakhale ngat ntchentche
Ey yo nokha mukudziwa, sasewela pa diwa
Tinapafunditsa pano agalu akujiwa
Kuyimba zokwiya, live bars kumango khiya
Deadly as they come, booth kusandutsa siwa
Skill ya a khiwa, upanga dolla palipose
Mafana mnadziwa amangolola chilichose
Sadziwa zoti sadziwa kalikose
Ndiana ndimadzimva kholo kulikose
Siine mfana watube, koma ndisiyeni ndizipope
Udolo ngat mose
Opanda ine, muli mmadzi
Nonse, siimunga ooloke
Kuwina mkwammagazi, simungandiloke
And i work hard, kangachepe bwanji
Sikabwela kokha
Olo uta talka, Suzandimva kufooka
Nde ukuti bwaaa, iwe ndine kape mndani
Ukufuna chaaa, mesa umati ndife adani
I know you listening
Mfana ndimvetsetse
Mfana khala chete
Usakhalee ngat ntchentche
I know you listening
Mfana ndimvetsetse
Mfana khala chete
Usakhalee ngat ntchentche
I heard you talking
Nigga you wanna know me
I heard you talking
Nigga you wanna know me
I know you listening
Mfana ndimvetsetse
Mfana khala chete
Usakhalee ngat ntchentche
I know you listening
Mfana ndimvetsetse
Mfana khala chete
Usakhalee ngat ntchentche