Hane kubanja choka samachoka choncho
Hane pochoka ngati mukuthawa nkhondo
(Hane wapambana)
Ndikulira koto
(Hane wapambana)
Ndikulira koto
Hane kubanja choka samachoka choncho
Hane pochoka anasiya mpoto pa moto
(Hane wapambana)
Ndikulira koto
(Hane wapambana)
Issh koma Hane
Hane
Hane wapambana
Ndikulira Hane
Hane wapambana
Issh koma Hane
Hane
Hane wapambana
Ndikulira Hane
Hane wapambana
Issh koma Hane
(Tay grin)
Oky
Rrrad
Ati bwanji apa
Issh koma Hane
Utangochoka
Nkhawa, Moti zoona unasiya anawa
Uli patsoka Mawa
Chozemba chimakumana nchokwawa
Unagulitsa ng'ombe zanga zonse
Napinyulitsa njinga zanga zonse
Kunabwelanso a bank nkhonde
Akuti unantapila chingongole
Eeh
Uli patsoka
Hane
Ndiwe njoka
Hane
Mimba m'tsekule ku joni ko
Hane
Ndalama zanga unapangila chiphaso
Issh koma
Hane
Hane
Hane wapambana
Ndikulira Hane
Hane wapambana
Issh koma Hane
Hane
Hane wapambana
Ndikulira Hane
Hane wapambana
Issh koma Hane