Your actions
Can tell me more
You can run away
But you can't hide from me
Komanso, Baby I know you more
I know when you mean it
And when you lie to me
Your actions speak louder
Maso pakamwa
Ndizo ziulura
Zonse wabisa
Your actions speak louder
Maso pakamwa
Ndizo ziulura
Zonse wabisa
Oky Ndamva
UsandiuzeNdamva
Zamuntima mwako Ndamva
Olo uzibise
Ndamva
Oky Ndamva
Usandiuze Ndamva
Zamuntima mwako Ndamva
Olo Uzibise
Ndamva
Ndamva
(Actions)
Ndamva
Ndamva
(Baby your actions)
Ndamva
Status
Ndimaikidwa yoona ndekha
I'll call you back
Ndimadikila
Call yosabwela
Oky ndamva
Nifumepo yapa Yanga nthawi yatha
It's over baby
Your actions speak louder
Maso pakamwa
Ndizo ziulura
Zonse wabisa
Your actions speak louder
Maso pakamwa
Ndizo ziulura
Zonse wabisa
Oky Ndamva
Usandiuze Ndamva
Zamuntima mwako Ndamva
Olo uzibise
Ndamva
Oky Ndamva
Usandiuze Ndamva
Zamuntima mwako Ndamva
Olo Uzibise
Ndamva
Ndamva
Takhala zaka zambiri
Muzowawa zokhoma awiri
When did I lose my lover
It's like as if I married a stranger
Simple things really matter
Ili kuti Romance ia
Ili kuti attention
Ali kuti ma plan aja
Okhe ndamva
Nifumepo yapa
Yang nthawi yatha
It's over baby your
Okhe ndamva
Nifumepo yapa
Yanga nthawi yatha
Yanga nthawi yatha!!