Back to Top

Spyral Mwenya - Ndimaganiza Bho Lyrics

Spyral Mwenya - Ndimaganiza Bho Lyrics

[ Featuring Gwamba, BeeJay, Barry Uno, Quest Mw ]

Ndimaganiza Bho Remix Lyrics

You thought I was done right?
But we just getting started!
Ife ndima yoh

(Pre-Chorus - Spyral Mwenya)
I got connects in every city and its clear
Get what i want and i want it, I don't care
Amangokakamila moto ndwa ifeyo (wa ifeyo!)
Mfana ochedwa pa zinthu sangakhale ineyo

(Chorus - Spyral Mwenya)
Ndimaganiza Bho Mani Mani
Ndimaganiza Bho Ndimaganiza Bho
Ndimaganiza Bho Mani Mani
Ndimaganiza Bho Ndimaganiza Bho
Ndimaganiza Bho (Shaaaa!)
Ndimaganiza Bho Ndimaganiza Bho
Ndimaganiza Bho Mani Mani
Ndimaganiza Bho Ndimaganiza Bho

(Verse 1 - Quest)
Nena ndi litilo, lomwe sinnaganize bho lo
Mboni ndi pillow, sindimaganizako slow yeah
Tryna make my money tall, I let my money talk
Uli m'maplani talka, ulibe plani choka (go go go go)
Oh my man i am just serious, ganiza mlingo opitilila
Nzeru zanga m'mazithilila, ganiza bho zikuphukila
Nnayiponya kutali ndipo sinnafike
I'm from Malawi singabalalike
Ganiza fine fine fine
I need the money, panga align ma deal ku signer signer signer
Show ndine headliner liner
I got connects got designers
Big leagues i'm not with minors
Call us the ghetto runners
Wakwiya azilume nsana

(Verse 2 - Bee Jay)
Yea Ya Ya (Mani Maniiiii)
Ye! usandipase GREEN kapena SPECIAL kapena SQUASH
Uzimixe kaye, paja ine ndiwama PUNCH
Ndipo akuzithemba ndiwowoo? Nkona ndikuwadya LUNCH
Pena ndimazidabwa kuti ndimaganiza BWANJI
Koma ndimaganiza ngati Gaba daily, ndimaganiza BHO (ball)
Iwe! sungaCashe kaMILLION umaganiza SLOW
Ndili ndi zima bomba mphwanga ndipo ndima NYUMWISA
Sinne mfana wa jonz koma ndiMAPHOURISA
Mpaka fanz ifileee, fike mawa matsileee
Ushashawu ndi wanga fanz ikuti Undipatsileee
Muzibaye vaccine verse yanga imaMiNITSA
Ndipo ine ndilibe target olo akazi ndimayimiSSa

(Chorus)

(Verse 3 - Spyral Mwenya)
Yeah yeh! Yeah yeh!
Ndimayiona bho (ball) uli mpila bwezi ine ndili Gaba
Funondigwetsa pansi koma akuchepela kaba
Now you wondering why the hommies calling me fada
I got relatives down from Jozi to Lusaka (la familia)
Lion stare on my face to show you i can be fierce
Got a golden mind is why i standout from my peers
Talking smack on your back, giving you these fake cheers
Hommies only act nice till you get what's better than theirs (prrapapapa)
Mfana wapa Malawi ndimalingalila kutali
Singakhale pa mbali ndimaganiza mwa machawi
Pomwe pali mbuzi pali nsuzi
Ndigwile mpeni 'ne ndiphe maluzi

(Verse 4 - Barry Uno)
Ndimaganiza bho, Jah Jah patsogolo bho
Pa ground sipali bho
Suzandipeza nkuyankhila zopusa pa social media no!
Suzamupeza Legendary BarryUno chasing clout for social media points
Suzamupeza akucheza ndi makape, mazoba osatha flow
Kutakata bho, huh
Kujagula bho, huh
Kugwilira no!
Mwa - muna omenya mkazi timulinganize timufake ma stones
Kupanga ignore huh
Kupanga ignore huh
Aneneri abo - dza
O - fu - na ku - tisocheresa kuti ife tikathere ku moto
All in all i mind my own, k'panga zondisangalasa, that Uno mode
That Mdub vibe, your very own, the legendary swag that sets the tone
Kutsogoza chikondi than live alone, kutsogoza umodzi so far, you are gone
In God we trust, he protects his own
Blessings on blessings, keep piling on

(Pre-Chorus)

(Verse 5 - Gwamba)
Ey yo Spyral! Yo!
Ndimaganiza bhooo heve nsanathoke'yi
Osati kumangotokota kuti ngini ikuchoke'yi
Munkati tivote mukazawina mutsitsa mafuta
Pano tikufa ndi njala inu ndikumaganiza mokhuta
Ndimaganiza prayer, long life ndi chi Mansion (eyiiih)
Anzanu akupanga ndalama inu 'ganizila tima caption (eyiiih)
Ndimaganiza Jah Jah, ndimamufila ndi passion (eyiiih)
Koma sindimangoganiza'ayi ndimayika action
Popanga za Yesu ndayika passion, zausatana ndayika ma sanction
Fusa Versace Richmond, Entwan yeh, za Yesu zalowa fashion
Ndili ndi Yesu zanga pheee
Ndili ndi Yesu zanga pheeeee!
[ Correct these Lyrics ]

[ Correct these Lyrics ]

We currently do not have these lyrics. If you would like to submit them, please use the form below.

Spyral Mwenya - Ndimaganiza Bho Video
(Show video at the top of the page)

Performed By: Spyral Mwenya
Featuring: Gwamba, BeeJay, Barry Uno, Quest Mw
Language: English
Length: 5:13

Tags:
No tags yet